Numeri 10:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anayamba kuyenda ambendera ya chigono cha ana a Yuda monga mwa magulu ao; woyang'anira gulu lake ndiye Nasoni mwana wa Aminadabu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anayamba kuyenda ambendera ya chigono cha ana a Yuda monga mwa magulu ao; woyang'anira gulu lake ndiye Nasoni mwana wa Aminadabu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Otsata mbendera ya zithando za fuko la Yuda ndiwo adayamba kunyamuka m'magulumagulu, ndipo mtsogoleri wa gulu lao anali Nasoni mwana wa Aminadabu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Magulu a msasa wa Yuda ndiwo anayamba kunyamuka potsata mbendera yawo. Mtsogoleri wa gulu lawo anali Naasoni mwana wa Aminadabu. Onani mutuwo |