Numeri 12:12 - Buku Lopatulika Asakhaletu iye ngati wakufa, amene dera lina la mnofu wake watha potuluka iye m'mimba mwa make. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Asakhaletu iye ngati wakufa, amene dera lina la mnofu wake watha potuluka iye m'mimba mwa make. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Musalole kuti Miriyamu akhale ngati mwana wobadwa wakufa, amene thupi lake lili loonongeka kumodzi.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Musalole kuti Miriamu akhale ngati mwana wobadwa wakufa kuchoka mʼmimba mwa amayi ake, thupi lake litawonongeka.” |
Ndipo Aroni anati kwa Mose, Mfumu yanga, musatiikiretu kuchimwa kumene tapusa nako, ndi kuchimwa nako.
Ndipo inu, pokhala akufa m'zolakwa ndi kusadulidwa kwa thupi lanu, anakupatsani moyo pamodzi ndi Iye, m'mene adatikhululukira ife zolakwa zonse;