Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 12:12 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Musalole kuti Miriamu akhale ngati mwana wobadwa wakufa kuchoka mʼmimba mwa amayi ake, thupi lake litawonongeka.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

12 Asakhaletu iye ngati wakufa, amene dera lina la mnofu wake watha potuluka iye m'mimba mwa make.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Asakhaletu iye ngati wakufa, amene dera lina la mnofu wake watha potuluka iye m'mimba mwa make.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Musalole kuti Miriyamu akhale ngati mwana wobadwa wakufa, amene thupi lake lili loonongeka kumodzi.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 12:12
9 Mawu Ofanana  

Kapena, bwanji sindinakwiriridwe pansi monga mwana wobadwa wakufa kale, ngati khanda limene silinaone kuwala kwa dzuwa?


Akhale ngati nkhono imene imasungunuka pamene ikuyenda; ngati mwana wakufa asanabadwe, iwo asaone dzuwa.


ndipo Aaroni anawuza Mose kuti, “Pepani mbuye wanga, musatilange chifukwa cha tchimo limene tachita mopusa.


Tsono Mose anafuwulira Yehova kuti, “Chonde Inu Mulungu, muchiritseni!”


Potsiriza pa onse anaonekeranso kwa ine, monga mwana wobadwa nthawi isanakwane.


Pamene munali akufa chifukwa cha machimo anu ndi osachita mdulidwe mʼmitima mwanu, Mulungu anakupatsani moyo mwa Khristu. Iye anatikhululukira machimo athu onse.


Koma mkazi wamasiye amene amangokhalira kuchita zosangalatsa moyo wake, wafa kale ngakhale akanali ndi moyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa