1 Akorinto 15:8 - Buku Lopatulika8 ndipo potsiriza pake pa onse, anaoneka kwa inenso monga mtayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 ndipo potsiriza pake pa onse, anaoneka kwa inenso monga mtayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Potsiriza, pambuyo pa onse adandiwonekeranso ineyo, ngakhale ndili ngati mpolo chabe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Potsiriza pa onse anaonekeranso kwa ine, monga mwana wobadwa nthawi isanakwane. Onani mutuwo |