Masalimo 58:8 - Buku Lopatulika8 Apite ngati nkhono yosungunuka; asaone dzuwa monga mtayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Apite ngati nkhono yosungunuka; asaone dzuwa monga mtayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Akhale ngati nkhonodambe imene imazimirira poyenda, ngati mtayo wosaona dzuŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Akhale ngati nkhono imene imasungunuka pamene ikuyenda; ngati mwana wakufa asanabadwe, iwo asaone dzuwa. Onani mutuwo |