Numeri 12:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Aroni anati kwa Mose, Mfumu yanga, musatiikiretu kuchimwa kumene tapusa nako, ndi kuchimwa nako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Aroni anati kwa Mose, Mfumu yanga, musatiikiretu kuchimwa kumene tapusa nako, ndi kuchimwa nako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Apo Aroni adauza Mose kuti, “Mbuyanga, musatilange chifukwa choti tachimwa, ndipo tachita zopusa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 ndipo Aaroni anawuza Mose kuti, “Pepani mbuye wanga, musatilange chifukwa cha tchimo limene tachita mopusa. Onani mutuwo |