Numeri 12:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo mtambo unachoka pachihema; ndipo taonani, Miriyamu anali wakhate, wa mbuu ngati chipale chofewa; ndipo Aroni anapenya Miriyamu, taonani, anali wakhate. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo mtambo unachoka pachihema; ndipo taonani, Miriyamu anali wakhate, wa mbu ngati chipale chofewa; ndipo Aroni anapenya Miriyamu, taonani, anali wakhate. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mtambo utachoka pamwamba pa chihema, Miriyamu adapezeka ali ndi khate lambuu ngati ufa, ndipo Aroni atacheuka, adangoona Miriyamu ali ndi khate. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pamene mtambo unachoka pamwamba pa Chihema, taonani, Miriamu anagwidwa ndi khate. Aaroni atachewuka anaona Miriamu ali ndi khate; Onani mutuwo |