Numeri 12:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Mose anafuulira kwa Yehova, ndi kuti, Mchiritsenitu, Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Mose anafuulira kwa Yehova, ndi kuti, Mchiritsenitu, Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsono mokweza mau Mose adauza Chauta kuti, “Mulungu ndikukupemphani kuti mumchiritse Miriyamu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Tsono Mose anafuwulira Yehova kuti, “Chonde Inu Mulungu, muchiritseni!” Onani mutuwo |