Masalimo 82:6 - Buku Lopatulika Ndinati Ine, Inu ndinu milungu, ndi ana a Wam'mwambamwamba nonsenu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndinati Ine, Inu ndinu milungu, ndi ana a Wam'mwambamwamba nonsenu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ine ndikuti, “Inu ndinu milungu, nonsenu ndinu ana a Mulungu Wopambanazonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Ndinati, ‘Inu ndinu Mulungu, nonsenu ndinu ana a Wammwambamwamba.’ |
Mlandu uliwonse wa cholakwa, kunena za ng'ombe, za bulu, za nkhosa, za chovala, za kanthu kalikonse kotayika, munthu anenako kali kake; mlandu wa onse awiri ufike kwa oweruza; iye amene oweruza amtsutsa alipe chowirikiza kwa mnansi wake.