Masalimo 82:7 - Buku Lopatulika7 Komatu mudzafa monga anthu, ndipo mudzagwa monga wina wa akulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Komatu mudzafa monga anthu, ndipo mudzagwa monga wina wa akulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Komabe mudzafa ngati anthu onse, ndipo mudzagwa ngati kalonga wina aliyense.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma mudzafa ngati anthu wamba; mudzagwa ngati wolamula wina aliyense.” Onani mutuwo |