Masalimo 82:6 - Buku Lopatulika6 Ndinati Ine, Inu ndinu milungu, ndi ana a Wam'mwambamwamba nonsenu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndinati Ine, Inu ndinu milungu, ndi ana a Wam'mwambamwamba nonsenu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ine ndikuti, “Inu ndinu milungu, nonsenu ndinu ana a Mulungu Wopambanazonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Ndinati, ‘Inu ndinu Mulungu, nonsenu ndinu ana a Wammwambamwamba.’ Onani mutuwo |