Masalimo 82:5 - Buku Lopatulika5 Sadziwa, ndipo sazindikira; amayendayenda mumdima; maziko onse a dziko lapansi agwedezeka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Sadziwa, ndipo sazindikira; amayendayenda mumdima; maziko onse a dziko lapansi agwedezeka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Iwo sadziŵa kanthu ndiponso alibe nzeru, amangoyenda m'chimbulimbuli. Maziko onse a dziko lapansi agwedezeka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 “Iwo sadziwa kanthu, sazindikira kalikonse. Amayendayenda mu mdima; maziko onse a dziko lapansi agwedezeka. Onani mutuwo |