Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 82:4 - Buku Lopatulika

4 Pulumutsani osauka ndi aumphawi; alanditseni m'dzanja la oipa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Pulumutsani osauka ndi aumphawi; alanditseni m'dzanja la oipa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 “Landitsani ofooka ndi osoŵa. Apulumutseni kwa anthu oipa.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Landitsani anthu ofowoka ndi osowa; apulumutseni mʼdzanja la anthu oyipa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 82:4
8 Mawu Ofanana  

Pakuti ndinapulumutsa wozunzika wakufuula; mwana wamasiye yemwe wosowa mthandizi.


Ndidziwa kuti Yehova adzanenera wozunzika mlandu, ndi kuweruzira aumphawi.


Yehova atero: Chitani chiweruzo ndi chilungamo, landitsani ofunkhidwa m'dzanja la wosautsa; musachite choipa, musamchitire mlendo chiwawa, kapena ana amasiye, kapena akazi amasiye, musakhetse mwazi wosachimwa pamalo pano.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa