Eksodo 22:28 - Buku Lopatulika28 Usapeputsa oweruza, kapena kutemberera mkulu wa anthu a mtundu wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Usapeputsa oweruza, kapena kutemberera mkulu wa anthu a mtundu wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 “Musanyoze Mulungu, ndipo musatemberere mtsogoleri wa anthu anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 “Musachite chipongwe Mulungu wanu kapena kutemberera mtsogoleri wa anthu anu. Onani mutuwo |