Eksodo 22:29 - Buku Lopatulika29 Usachedwa kuperekako zipatso zako zochuluka, ndi zothira zako. Woyamba wa ana ako aamuna undipatse Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Usachedwa kuperekako zipatso zako zochuluka, ndi zothira zako. Woyamba wa ana ako amuna undipatse Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 “Musachedwe kundipatsa zopereka zotapa pa zokolola zanu zambiri ndiponso pa vinyo wanu wochuluka. “Mundipatse ana anu achisamba aamuna. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 “Musachedwe kupereka kwa Ine zokolola zanu zochuluka ndi vinyo wanu wochuluka. “Mundipatse ana anu achisamba aamuna. Onani mutuwo |