Masalimo 82:4 - Buku Lopatulika Pulumutsani osauka ndi aumphawi; alanditseni m'dzanja la oipa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pulumutsani osauka ndi aumphawi; alanditseni m'dzanja la oipa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Landitsani ofooka ndi osoŵa. Apulumutseni kwa anthu oipa.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Landitsani anthu ofowoka ndi osowa; apulumutseni mʼdzanja la anthu oyipa. |
Yehova atero: Chitani chiweruzo ndi chilungamo, landitsani ofunkhidwa m'dzanja la wosautsa; musachite choipa, musamchitire mlendo chiwawa, kapena ana amasiye, kapena akazi amasiye, musakhetse mwazi wosachimwa pamalo pano.