Masalimo 78:2 - Buku Lopatulika Ndidzatsegula pakamwa panga mofanizira; ndidzatchula zinsinsi zoyambira kale. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndidzatsegula pakamwa panga mofanizira; ndidzatchula zinsinsi zoyambira kale. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndidzakusimbirani fanizo. Ndidzalankhula nkhani zobisika zakalekale, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndidzatsekula pakamwa panga mʼmafanizo, ndidzayankhula zinthu zobisika, zinthu zakalekale |
Kumbukirani zinthu zoyamba zakale, kuti Ine ndine Mulungu, ndipo palibenso wina; Ine ndine Mulungu, ndipo palibenso wina wofanana ndi Ine;
ndipo sanalankhule nao wopanda fanizo: koma m'tseri anatanthauzira zonse kwa ophunzira ake.
Ndipo Yehova anawazula m'nthaka mwao mokwiya ndi mozaza, ndi mu ukali waukulu, nawaponya m'dziko lina, monga lero lino.