Masalimo 49:4 - Buku Lopatulika4 Ndidzatchera khutu kufanizo, ndidzafotokozera chophiphiritsa changa poimbira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndidzatchera khutu kufanizo, ndidzafotokozera chophiphiritsa changa poimbira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndidzakupherani mwambi, ndidzamasulira tanthauzo lake poimba pangwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndidzatchera khutu langa ku mwambo, ndi pangwe ndidzafotokoza momveka mwambi wanga. Onani mutuwo |