Masalimo 49:3 - Buku Lopatulika3 Pakamwa panga padzanena zanzeru; ndipo chilingiriro cha mtima wanga chidzakhala cha chidziwitso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakamwa panga padzanena zanzeru; ndipo chilingiriro cha mtima wanga chidzakhala cha chidziwitso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Zosinkhasinkha za mtima wanga zidzakhala zakuya, ndipo ndidzalankhula zanzeru. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pakamwa panga padzayankhula mawu anzeru; mawu ochokera mu mtima mwanga adzapereka nzeru. Onani mutuwo |