Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 49:2 - Buku Lopatulika

2 awamba ndi omveka omwe, achuma ndi aumphawi omwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 awamba ndi omveka omwe, achuma ndi aumphawi omwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 anthu otsika ndi okwera omwe, olemera ndi osauka omwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 anthu wamba pamodzi ndi anthu odziwika, olemera pamodzinso ndi osauka:

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 49:2
10 Mawu Ofanana  

Nanga kwa Iye wosasamalira nkhope za akalonga, wosasiyanitsa pakati pa wolemera ndi wosauka? Pakuti onsewo ndiwo ntchito ya manja ake.


Indetu, anthu achabe ndi mpweya, ndipo anthu aakulu ndi bodza, pakuwayesa apepuka; onse pamodzi apepuka koposa mpweya.


Wolemera ndi wosauka akumana, wolenga onsewo ndiye Yehova.


Idzani pafupi, amitundu inu, kuti mumve; mverani anthu inu, dziko ndi zinthu zonse zotulukamo.


Imvani, mitundu ya anthu, inu nonse; tamvera, dziko lapansi, ndi zonse zili m'mwemo; ndipo Ambuye Yehova akhale mboni yakutsutsa inu, Ambuye mu Kachisi wake wopatulika.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa