Masalimo 49:5 - Buku Lopatulika5 Ndidzaoperanji masiku oipa, pondizinga amphulupulu onditsata kuchidendene? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndidzaoperanji masiku oipa, pondizinga amphulupulu onditsata kuchidendene? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ndichitirenji mantha pa nthaŵi yamavuto pamene anthu ondizunza akundizinga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ine ndichitirenji mantha pamene masiku oyipa afika, pamene achinyengo oyipa andizungulira. Onani mutuwo |