Masalimo 49:6 - Buku Lopatulika6 Iwo akutama kulemera kwao; nadzitamandira pa kuchuluka kwa chuma chao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Iwo akutama kulemera kwao; nadzitamandira pa kuchuluka kwa chuma chao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Anthu otero amangokhulupirira chuma chao, amanyada chifukwa ali ndi chuma chambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iwo amene adalira kulemera kwawo ndi kutamandira kuchuluka kwa chuma chawo? Onani mutuwo |