Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 49:7 - Buku Lopatulika

7 kuombola mbale sangadzamuombole, kapena kumperekera dipo kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 kuombola mbale sangadzamuombole, kapena kumperekera dipo kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Zoonadi, palibe munthu amene angadziwombole, kapena kupatsa Mulungu mtengo wa moyo wake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Palibe munthu amene angawombole moyo wa mnzake kapena kuperekera mnzake dipo kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 49:7
10 Mawu Ofanana  

Nawawerengera Hamani kulemera kwake kwakukulu, ndi ana ake ochuluka, ndi zonse mfumu idamkuza nazo, ndi umo adamkweza koposa akalonga ndi anyamata a mfumu.


Chuma cha wolemera ndicho mzinda wake wolimba; alingalira kuti ndicho khoma lalitali.


Nenani, atero Yehova, Mitembo yathu idzagwa ngati ndowe pamunda, ndi monga chipukutu pambuyo pa wakusenga, palibe wochitola.


Koma Ine ndine Yehova Mulungu wako chichokere dziko la Ejipito, ndidzakukhalitsanso m'mahema, monga masiku a zikondwerero zoikika.


Pakuti munthu adzapindulanji, akalandira dziko lonse, nataya moyo wake? Kapena munthu adzaperekanji chosintha ndi moyo wake?


monga Mwana wa Munthu sanadze kutumikiridwa koma kutumikira, ndi kupereka moyo wake dipo la anthu ambiri.


Koma ochenjera anayankha nati, Kapena sangakwanire ife ndi inu; koma makamaka mukani kwa ogulitsa malonda, mukadzigulire inu nokha.


Pakuti munthu akapereka chiyani chosintha nacho moyo wake?


amene anadzipereka yekha chiombolo m'malo mwa onse; umboni m'nyengo zake;


podziwa kuti simunaomboledwa ndi zovunda, golide ndi siliva, kusiyana nao makhalidwe anu achabe ochokera kwa makolo anu:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa