Masalimo 49:8 - Buku Lopatulika8 Popeza chiombolo cha moyo wao ncha mtengo wake wapatali, ndipo chilekeke nthawi zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Popeza chiombolo cha moyo wao ncha mtengo wake wapatali, ndipo chilekeke nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Popeza kuti choombolera moyo wa munthu ndi chamtengowapatali, ndipo sangathe kuchikwanitsa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Dipo la moyo ndi la mtengowapatali, palibe malipiro amene angakwanire, Onani mutuwo |