Masalimo 49:9 - Buku Lopatulika9 Kuti akhale ndi moyo osafa, osaona chivundi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Kuti akhale ndi moyo osafa, osaona chivundi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 kuti azikhalabe ndi moyo mpaka muyaya osapita ku manda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 kuti iye akhale ndi moyo mpaka muyaya ndi kusapita ku manda. Onani mutuwo |