Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 78:3 - Buku Lopatulika

3 Zimene tinazimva, ndi kuzidziwa, ndipo makolo athu anatifotokozera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Zimene tinazimva, ndi kuzidziwa, ndipo makolo athu anatifotokozera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 zinthu zimene tidazimva ndi kuzidziŵa, zomwe makolo athu adatifotokozera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 zimene tinazimva ndi kuzidziwa, zimene makolo athu anatiwuza.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:3
9 Mawu Ofanana  

Taonani, diso langa lachiona chonsechi; m'khutu mwanga ndachimva ndi kuchizindikira.


Mbadwo wina udzalemekezera ntchito zanu mbadwo unzake, ndipo udzalalikira zamphamvu zanu.


Mulungu, tidamva m'makutu mwathu, makolo athu anatisimbira, za ntchitoyo mudaichita masiku ao, masiku akale.


Monga tidamva, momwemo tidapenya m'mzinda wa Yehova wa makamu, m'mzinda wa Mulungu wathu, Mulungu adzaukhazikitsa kunthawi yamuyaya.


ndi kuti ufotokozere m'makutu a ana ako, ndi a zidzukulu zako, chomwe ndidzachita mu Ejipito, ndi zizindikiro zanga zimene ndinaziika pakati pao; kuti mudziwe kuti Ine ndine Yehova.


Ndipo ukauze mwana wako wamwamuna tsikulo, ndi kuti, Nditero chifukwa chomwe Yehova anandichitira ine potuluka ine mu Ejipito.


Wamoyo, wamoyo, iye adzakuyamikani inu, monga ine lero; Atate adzadziwitsa ana ake zoona zanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa