Masalimo 78:2 - Buku Lopatulika2 Ndidzatsegula pakamwa panga mofanizira; ndidzatchula zinsinsi zoyambira kale. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndidzatsegula pakamwa panga mofanizira; ndidzatchula zinsinsi zoyambira kale. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndidzakusimbirani fanizo. Ndidzalankhula nkhani zobisika zakalekale, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndidzatsekula pakamwa panga mʼmafanizo, ndidzayankhula zinthu zobisika, zinthu zakalekale Onani mutuwo |