Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 4:34 - Buku Lopatulika

34 ndipo sanalankhule nao wopanda fanizo: koma m'tseri anatanthauzira zonse kwa ophunzira ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 ndipo sanalankhule nao wopanda fanizo: koma m'tseri anatanthauzira zonse kwa ophunzira ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Sankaŵaphunzitsa popanda mafanizo. Koma ankati akakhala payekha ndi ophunzira ake, ankaŵatanthauzira zonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Iye sananene kanthu kwa iwo osagwiritsa ntchito fanizo. Koma ali yekha ndi ophunzira ake, ankawatanthauzira zonse.

Onani mutuwo Koperani




Marko 4:34
12 Mawu Ofanana  

Zonsezi Yesu anaziphiphiritsira m'mafanizo kwa makamu a anthu; ndipo kopanda fanizo sanalankhule kanthu kwa iwo;


Ndipo pamene anakhala pa yekha, iwo amene anali pafupi ndi Iye pamodzi ndi khumi ndi awiriwo anamfunsa za mafanizo.


Ndipo ndi mafanizo otere ambiri analankhula nao mau, monga anakhoza kumva;


Ndipo anayamba kwa Mose, ndi kwa aneneri onse nawatanthauzira iwo m'malembo onse zinthu za Iye yekha.


Fanizo ili Yesu ananena kwa iwo; koma sanazindikire zimene Yesu analikulankhula nao.


Zinthu izi ndalankhula ndi inu m'mafanizo; ikudza nthawi imene sindidzalankhula ndi inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu momveka za Atate.


Ndipo pamene adampangira tsiku, anadza kunyumba yake anthu ambiri; amenewo anawafotokozera, ndi kuchitira umboni Ufumu wa Mulungu, ndi kuwakopa za Yesu, zochokera m'chilamulo cha Mose ndi mwa aneneri, kuyambira mamawa kufikira madzulo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa