Marko 4:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo ndi mafanizo otere ambiri analankhula nao mau, monga anakhoza kumva; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo ndi mafanizo otere ambiri analankhula nao mau, monga anakhoza kumva; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Yesu ankaphunzitsa anthu ndi mafanizo ambiri onga ameneŵa, polinganiza ndi nzeru za anthuwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Ndi mafanizo ambiri onga awa Yesu anayankhula mawu kwa iwo, monga mmene akanatha kumvetsa. Onani mutuwo |