Adzikhazikitsa mafumu a dziko lapansi, nachita upo akulu pamodzi, Kutsutsana naye Yehova, ndi Wodzozedwa wake, ndi kuti,
Masalimo 48:5 - Buku Lopatulika Anapenya mudziwo, ndipo pamenepo anadabwa; anaopsedwa, nathawako. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Anapenya mudziwo, ndipo pamenepo anadabwa; anaopsedwa, nathawako. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Atangopenya mzindawo adadzidzimuka, adachita mantha, nathaŵa chinambalala. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero iwo anaona mzindawo ndipo anadabwa kwambiri; anathawa ndi mantha aakulu. |
Adzikhazikitsa mafumu a dziko lapansi, nachita upo akulu pamodzi, Kutsutsana naye Yehova, ndi Wodzozedwa wake, ndi kuti,
Ndipo anagulula njinga za magaleta ao, nawayendetsa molemetsa; pamenepo Aejipito anati, Tithawe pamaso pa Israele; pakuti Yehova alikuwagwirira nkhondo pa Aejipito.
Ndipo mafumu awa onse anasonkhana, nadza namanga pamodzi ku madzi a Meromu, kumthira Israele nkhondo.