Yoswa 11:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo mafumu awa onse anasonkhana, nadza namanga pamodzi ku madzi a Meromu, kumthira Israele nkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo mafumu awa onse anasonkhana, nadza namanga pamodzi ku madzi a Meromu, kumthira Israele nkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mafumu onseŵa adasonkhana pamodzi, nakamanga zithando ku mtsinje wa Meromu, kuti alimbane ndi Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mafumu onsewa anasonkhana pamodzi ndipo anamanga misasa yawo ku mtsinje wa Meromu, kuti amenyane ndi Israeli. Onani mutuwo |