Eksodo 14:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo anagulula njinga za magaleta ao, nawayendetsa molemetsa; pamenepo Aejipito anati, Tithawe pamaso pa Israele; pakuti Yehova alikuwagwirira nkhondo pa Aejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo anagulula njinga za magaleta ao, nawayendetsa molemetsa; pamenepo Aejipito anati, Tithawe pamaso pa Israele; pakuti Yehova alikuwagwirira nkhondo pa Aejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Adapinda mikombero ya magaleta ao, kotero kuti magaletawo ankayenda movutika. Pamenepo Aejipito aja adati, “Tiyeni tiŵathaŵe Aisraeleŵa, chifukwa Chauta akuŵamenyera nkhondo, kulimbana nafe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Yehova anamanga matayala a magaleta kotero kuti ankavutika kuyenda. Ndipo Aigupto anati, “Tiyeni tiwathawe Aisraeli! Yehova akuwamenyera nkhondo kulimbana nafe.” Onani mutuwo |