Wodala munthuyo wosayenda mu uphungu wa oipa, kapena wosaimirira m'njira ya ochimwa, kapena wosakhala pansi pa bwalo la onyoza.
Masalimo 26:5 - Buku Lopatulika Ndidana nao msonkhano wa ochimwa, ndipo sindidzakhala nao pansi ochita zoipa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndidana nao msonkhano wa ochimwa, ndipo sindidzakhala nao pansi ochita zoipa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndimadana ndi anthu ochita zoipa, sindikhala pamodzi ndi anthu oipa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndimanyansidwa ndi msonkhano wa anthu ochita zoyipa ndipo ndimakana kukhala pansi pamodzi ndi oyipa. |
Wodala munthuyo wosayenda mu uphungu wa oipa, kapena wosaimirira m'njira ya ochimwa, kapena wosakhala pansi pa bwalo la onyoza.