Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 26:6 - Buku Lopatulika

6 Ndidzasamba manja anga mosalakwa; kuti ndizungulire guwa la nsembe lanu, Yehova;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndidzasamba manja anga mosalakwa; kuti ndizungulire guwa la nsembe lanu, Yehova;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ndimasamba m'manja kuwonetsa kuti sindidachimwe, ndimakupembedzani pa guwa lanu lansembe, Inu Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Ndimasamba mʼmanja mwanga kuonetsa kusalakwa kwanga ndi kupita kukatumikira pa guwa lanu la nsembe, Inu Yehova,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 26:6
13 Mawu Ofanana  

Woyera m'manja, ndi woona m'mtima, ndiye; iye amene sanakweze moyo wake kutsata zachabe, ndipo salumbira monyenga.


Kuti ndipite kufikira guwa la nsembe la Mulungu, kufikira Mulungu wa chimwemwe changa chenicheni, ndi kuti ndikuyamikeni ndi zeze, Mulungu, Mulungu wanga.


Indedi, ndinayeretsa mtima wanga kwachabe, ndipo ndinasamba m'manja mosalakwa.


Simoni Petro ananena ndi Iye, Ambuye, si mapazi anga okha, komanso manja ndi mutu.


Ndipo akulu onse a mzindawo wokhala pafupi pa munthu wophedwayo azisamba manja ao pa ng'ombeyo yodulidwa khosi m'chigwamo;


Chifukwa chake ndifuna kuti amunawo apemphere pamalo ponse, ndi kukweza manja oyera, opanda mkwiyo ndi makani.


zosati zochokera m'ntchito za m'chilungamo, zimene tidazichita ife, komatu monga mwa chifundo chake anatipulumutsa ife, mwa kutsuka kwa kubadwanso ndi makonzedwe a Mzimu Woyera,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa