Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 26:7 - Buku Lopatulika

7 kuti ndimveketse mau a chiyamiko, ndi kulalikira ntchito zanu zonse zozizwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 kuti ndimveketse mau a chiyamiko, ndi kulalikira ntchito zanu zonse zozizwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ndimaimba molimbika nyimbo yothokozera, ndimalalika ntchito zanu zonse zodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 kulengeza mofuwula za matamando anu ndi kuwuza onse za ntchito zanu zodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 26:7
23 Mawu Ofanana  

Fotokozerani ulemerero wake mwa amitundu, zodabwitsa zake mwa mitundu yonse ya anthu.


Muimbireni, muimbireni zomlemekeza; fotokozerani zodabwitsa zake zonse.


Nditsegulireni zipata za chilungamo; ndidzalowamo, ndidzayamika Yehova.


Yehova ndiye Mulungu, amene anatiunikira; mangani nsembe ndi zingwe, kunyanga za guwa la nsembe.


Mundizindikiritse njira ya malangizo anu; kuti ndilingalire zodabwitsa zanu.


Kwezani manja anu kumalo oyera, nimulemekeze Yehova.


Ndidzalingalira ulemerero waukulu wa ulemu wanu, ndi ntchito zanu zodabwitsa.


Wolemekezeka Yehova Mulungu, Mulungu wa Israele, amene achita zodabwitsa yekhayo.


Ndidzayamika Yehova ndi mtima wanga wonse; ndidzawerengera zodabwitsa zanu zonse.


Kuti ndibukitse lemekezo lanu lonse; pa bwalo la mwana wamkazi wa Ziyoni, ndidzakondwera nacho chipulumutso chanu.


Ndidzakondwerera ndi kusekera mwa Inu; ndidzaimbira dzina lanu, Wam'mwambamwamba Inu.


Tidze nacho chiyamiko pamaso pake, timfuulire Iye mokondwera ndi nyimbo.


Ndipo atamletsa kuyamwa anakwera naye, pamodzi ndi ng'ombe ya zaka zitatu, ndi efa wa ufa, ndi thumba la vinyo, nafika naye kunyumba ya Yehova ku Silo; koma mwanayo anali wamng'ono.


Ndinampempha mwanayu; ndipo Yehova anandipatsa chopempha changa ndinachipempha kwa Iye;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa