Masalimo 26:8 - Buku Lopatulika8 Yehova, ndikonda chikhalidwe cha nyumba yanu, ndi malo akukhalamo ulemerero wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Yehova, ndikonda chikhalidwe cha nyumba yanu, ndi malo akukhalamo ulemerero wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Inu Chauta, ndimakonda Nyumba imene mumakhalamo, ndiye kuti malo amene kuli ulemerero wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndimakonda Nyumba imene Inu Yehova mumakhalamo, malo amene ulemerero wanu umapezekako. Onani mutuwo |