Masalimo 26:5 - Buku Lopatulika5 Ndidana nao msonkhano wa ochimwa, ndipo sindidzakhala nao pansi ochita zoipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndidana nao msonkhano wa ochimwa, ndipo sindidzakhala nao pansi ochita zoipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ndimadana ndi anthu ochita zoipa, sindikhala pamodzi ndi anthu oipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ndimanyansidwa ndi msonkhano wa anthu ochita zoyipa ndipo ndimakana kukhala pansi pamodzi ndi oyipa. Onani mutuwo |