Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 26:4 - Buku Lopatulika

4 Sindinakhala pansi ndi anthu achabe; kapena kutsagana nao anthu othyasika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Sindinakhala pansi ndi anthu achabe; kapena kutsagana nao anthu othyasika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Sindikhala pamodzi ndi anthu onyenga, sindiyenda ndi anthu achiphamaso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ine sindikhala pansi pamodzi ndi anthu achinyengo, kapena kufunsa nzeru kwa achiphamaso.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 26:4
11 Mawu Ofanana  

Ngati ndinayanjana nalo bodza, ndi phazi langa linathamangira chinyengo;


Wodala munthuyo wosayenda mu uphungu wa oipa, kapena wosaimirira m'njira ya ochimwa, kapena wosakhala pansi pa bwalo la onyoza.


Mtima wopulukira udzandichokera; sindidzadziwana naye woipa.


Mundichokere ochita zoipa inu; kuti ndisunge malamulo a Mulungu wanga.


Ine ndine wakuyanjana nao onse akukuopani, ndi iwo akusamalira malangizo anu.


Zakudya zikwanira wolima minda yake; koma wotsata anthu opanda pake asowa nzeru.


Ukayenda ndi anzeru udzakhala wanzeru: koma mnzao wa opusa adzaphwetekedwa.


Lekani, achibwana inu, nimukhale ndi moyo; nimuyende m'njira ya nzeru.


Sindinakhala m'msonkhano wa iwo amene asekerasekera, ndi kusangalala; ndinakhala pandekha chifukwa cha dzanja lanu; pakuti mwandidzaza ndi mkwiyo.


Musanyengedwe; mayanjano oipa aipsa makhalidwe okoma.


Chifukwa chake, Tulukani pakati pao, ndipo patukani, ati Ambuye, Ndipo musakhudza kanthu kosakonzeka; ndipo Ine ndidzalandira inu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa