Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 31:6 - Buku Lopatulika

6 Ndikwiya nao iwo akusamala zachabe zonama, koma ndikhulupirira Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndikwiya nao iwo akusamala zachabe zonama, koma ndikhulupirira Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Inu mumadana ndi opembedza mafano achabechabe. Koma ine ndimakhulupirira Inu Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Koma ine ndimadana nawo amene amamamatira mafano achabechabe; ine ndimadalira Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 31:6
13 Mawu Ofanana  

Inu mudziwa kukhala kwanga ndi kuuka kwanga, muzindikira lingaliro langa muli kutali.


Woyera m'manja, ndi woona m'mtima, ndiye; iye amene sanakweze moyo wake kutsata zachabe, ndipo salumbira monyenga.


Ndidana nao msonkhano wa ochimwa, ndipo sindidzakhala nao pansi ochita zoipa.


fumbi ndi kubwera pansi pomwe linali kale, mzimu ndi kubwera kwa Mulungu amene anaupereka.


Ndiwo chabe, ndiwo chiphamaso; pa nthawi ya kulangidwa kwao adzatha.


Koma onse pamodzi apulukira ndi kupusa; mtengo ndiwo chilangizo, chopanda pake.


Iwo osamalira mabodza opanda pake ataya chifundo chaochao.


Ndipo ananena nao, Tungani tsopano, mupite nao kwa mkulu wa phwando. Ndipo anapita nao.


chifukwa kuti, ngakhale anadziwa Mulungu, sanamchitire ulemu wakuyenera Mulungu, ndipo sanamyamike; koma anakhala opanda pake m'maganizo ao, ndipo unada mtima wao wopulukira.


Koma nditi kuti zimene amitundu apereka nsembe azipereka kwa ziwanda osati kwa Mulungu; ndipo sindifuna kuti inu muyanjane ndi ziwanda.


Tsono kunena za kudya zoperekedwa nsembe kwa mafano, tidziwa kuti fano silili kanthu padziko lapansi, ndi kuti palibe Mulungu koma mmodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa