Luka 24:3 - Buku Lopatulika Ndipo m'mene analowa sanapeze mtembo wa Ambuye Yesu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo m'mene analowa sanapeze mtembo wa Ambuye Yesu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adaloŵa m'mandamo koma sadaupeze mtembo wa Ambuye Yesu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo atalowamo sanapeze mtembo wa Ambuye Yesu. |
ndipo m'mene sanapeze mtembo wake, anadza, nanena kuti adaona m'masomphenya angelo, amene ananena kuti ali ndi moyo Iye.
Ndipo pamene Ambuye anamuona, anagwidwa ndi chifundo chifukwa cha iye, nanena naye, Usalire.
Potero kuyenera kuti wina wa amunawo anatsatana nafe nthawi yonseyi Ambuye Yesu analowa natuluka mwa ife,