Luka 24:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo kunali, m'mene anathedwa nzeru nacho, taonani amuna awiri anaimirira pafupi pao atavala zonyezimira; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo kunali, m'mene anathedwa nzeru nacho, taonani amuna awiri anaimirira pafupi pao atavala zonyezimira; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Akadali othedwa nzeru choncho pa zimenezo, adangoona anthu aŵiri ovala zovala zonyezimira ataimirira pafupi ndi iwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pamene iwo ankadabwa za zimenezi, mwadzidzidzi, amuna awiri ovala zovala zonyezimira kwambiri anayimirira pambali pawo. Onani mutuwo |