Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 24:3 - Buku Lopatulika

3 Ndipo m'mene analowa sanapeze mtembo wa Ambuye Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo m'mene analowa sanapeze mtembo wa Ambuye Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Adaloŵa m'mandamo koma sadaupeze mtembo wa Ambuye Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 ndipo atalowamo sanapeze mtembo wa Ambuye Yesu.

Onani mutuwo Koperani




Luka 24:3
6 Mawu Ofanana  

Ndipo ophunzira anadza kutsidya linalo, naiwala kutenga mikate.


Ndipo anapeza mwala unakunkhunizidwa kuuchotsa pamanda.


ndipo m'mene sanapeze mtembo wake, anadza, nanena kuti adaona m'masomphenya angelo, amene ananena kuti ali ndi moyo Iye.


Ndipo pamene Ambuye anamuona, anagwidwa ndi chifundo chifukwa cha iye, nanena naye, Usalire.


Potero kuyenera kuti wina wa amunawo anatsatana nafe nthawi yonseyi Ambuye Yesu analowa natuluka mwa ife,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa