Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 16:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo ophunzira anadza kutsidya linalo, naiwala kutenga mikate.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo ophunzira anadza kutsidya linalo, naiwala kutenga mikate.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Pamene ophunzira aja adakafika kutsidya, anali ataiŵala kutenga buledi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Koma atawoloka nyanja, ophunzira anayiwala kutenga buledi.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 16:5
4 Mawu Ofanana  

Ndipo m'mene Iye anauza makamuwo amuke, analowa m'ngalawa, nafika m'malire a Magadani.


Obadwa oipa ndi achigololo afunafuna chizindikiro; ndipo sadzalandira chizindikiro china, koma chizindikiro cha Yona. Ndipo Iye anawasiya, nachokapo.


Ndipo Yesu anati kwa iwo, Yang'anirani mupewe chotupitsa mkate cha Afarisi ndi Asaduki.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa