Mateyu 16:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Yesu anati kwa iwo, Yang'anirani mupewe chotupitsa mkate cha Afarisi ndi Asaduki. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Yesu anati kwa iwo, Yang'anirani mupewe chotupitsa mkate cha Afarisi ndi Asaduki. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Yesu adaŵauza kuti, “Muchenjere nacho chofufumitsira buledi cha Afarisi ndi Asaduki.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Yesu anawawuza kuti, “Chenjerani, khalani tcheru ndi yisiti wa Afarisi ndi Asaduki.” Onani mutuwo |