Mateyu 16:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo iwo anafunsana wina ndi mnzake, nati, Sitinatenge mikate. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo iwo anafunsana wina ndi mnzake, nati, Sitinatenga mikate. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Apo ophunzirawo adayamba kukambirana nkumati, “Akuterotu chifukwa sitidatenge buledi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iwo anakambirana pakati pawo za izi ndipo anati, “Ichi nʼchifukwa chakuti sitinatenge buledi aliyense.” Onani mutuwo |