Mateyu 16:8 - Buku Lopatulika8 Koma Yesu, m'mene anadziwa, anati, Ha, inu okhulupirira pang'ono, mufunsana chifukwa ninji wina ndi mnzake, kuti simunatenga mikate? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma Yesu, m'mene anadziwa, anati, Ha, inu okhulupirira pang'ono, mufunsana chifukwa ninji wina ndi mnzake, kuti simunatenga mikate? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Yesu adaadziŵa zimene iwo ankanena. Ndiye adaŵafunsa kuti, “Bwanji mukukambirana zakuti mulibe buledi, inu a chikhulupiriro chochepanu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yesu atadziwa zokambirana zawo, anawafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mukukambirana zakuti, ‘mulibe buledi?’ Inu achikhulupiriro chochepa. Onani mutuwo |