Mateyu 16:9 - Buku Lopatulika9 Kodi chikhalire simudziwa, ndipo simukumbukira mikate isanu ija ya anthu aja zikwi zisanu, ndi madengu angati munawatola? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Kodi chikhalire simudziwa, ndipo simukumbukira mikate isanu ija ya anthu aja zikwi zisanu, ndi madengu angati munawatola? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kodi mpaka pano simunamvetsebe? Kodi simukukumbukira kuti ndi buledi msanu ndidadyetsa anthu zikwi zisanu? Nanga mudaadzaza madengu angati ndi zotsala? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kodi inu simukumvetsetsabe? Kodi simukukumbukira za buledi musanu amene anadya anthu 5,000 ndi madengu amene munadzaza? Onani mutuwo |