Mateyu 16:10 - Buku Lopatulika10 Penanso mikate isanu ndi iwiri ija ya anthu zikwi zinai, ndi madengu angati munawatola? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Penanso mikate isanu ndi iwiri ija ya anthu zikwi zinai, ndi madengu angati munawatola? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Sujanso ndi buledi msanu ndi muŵiri ndidadyetsa anthu zikwi zinai? Nanga mudaadzaza madengu angati a zotsala? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Kapena buledi musanu ndi muwiri amene anadya anthu 4,000, nanga ndi madengu angati amene munadzaza? Onani mutuwo |