Mateyu 16:11 - Buku Lopatulika11 Bwanji nanga simudziwa kuti sindinanena kwa inu za mikate? Koma pewani chotupitsa cha Afarisi ndi Asaduki. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Bwanji nanga simudziwa kuti sindinanena kwa inu za mikate? Koma pewani chotupitsa cha Afarisi ndi Asaduki. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Nanga bwanji simukuzindikira kuti sindimanena za buledi? Chenjera nachoni chofufumitsira buledi cha Afarisi ndi Asaduki.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Zitheka bwanji kuti inu simukumvetsetsa kuti Ine sindinkayankhula nanu za buledi? Koma inu chenjerani ndi yisiti wa Afarisi ndi Asaduki.” Onani mutuwo |