Mateyu 16:12 - Buku Lopatulika12 Pomwepo anadziwitsa kuti sanawauze kupeza chotupitsa cha mikate, koma chiphunzitso cha Afarisi ndi Asaduki. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pomwepo anadziwitsa kuti sanawauze kupeza chotupitsa cha mikate, koma chiphunzitso cha Afarisi ndi Asaduki. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pamenepo iwo adazindikira kuti Yesu sankaŵauza kuti achenjere ndi chofufumitsira buledi, koma kuti achenjere ndi zophunzitsa za Afarisi ndi Asaduki. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kenaka iwo anazindikira kuti Iye samawawuza kuti achenjere ndi yisiti wa buledi koma ndi chiphunzitso cha Afarisi ndi Asaduki. Onani mutuwo |